Ku nyasa ngati mphonongolo ya Satana.
Kwanu mukadya zokazinga ndi chimanga
Kwanu ndinu osauka kuti katundu wonse ndiwojambula
Big man yanu inkagwila ntchito kwa mwenye. Atayiwuza “Get out “ inapita panja kukazula gate.
Kwanu mukadya zamu container ndi malambe
Kuwonda konseko kumachita kuzinda mvula
Kuda kwambili mpakana utabeleka mwana anayamba kutcholela amawona ngati ndi madzulo
You can follow @daniel_smph.
Tip: mention @twtextapp on a Twitter thread with the keyword “unroll” to get a link to it.

Latest Threads Unrolled: